Description:... Kutsatira Mulungu ndi ulendo wosangalatsa wopeza zinthu. Kutsatira ndi kutengera anthu ena ndi luso lachikale lophunzirira lomwe Yesu Khristu anasankha ngati njira yaikulu yophunzitsira. M’malo mochita manyazi ndi njira yoyesedwa ndi nthawiyi, ndi nthawi yomvetsetsa kukongola ndi kudzichepetsa kwa luso la kutsatira.Mu bukhuli, muzapeza yemwe, chomwe ndi momwe mungatsatire moyenerera. Bukhu lopambana latsopanoli lolembedwa ndi Dag Heward-Mills lipereka luso la kutsatira malo ake oyenerera mu zokumana zathu za Chikhristu.
Kutsatira Mulungu ndi ulendo wosangalatsa wopeza zinthu. Kutsatira ndi kutengera anthu ena ndi luso lachikale lophunzirira lomwe Yesu Khristu anasankha ngati njira yaikulu yophunzitsira. M’malo mochita manyazi ndi njira yoyesedwa ndi nthawiyi, ndi nthawi yomvetsetsa kukongola ndi kudzichepetsa kwa luso la kutsatira.
Mu bukhuli, muzapeza yemwe, chomwe ndi momwe mungatsatire moyenerera. Bukhu lopambana latsopanoli lolembedwa ndi Dag Heward-Mills lipereka luso la kutsatira malo ake oyenerera mu zokumana zathu za Chikhristu.
به شما اطمینان می دهیم در کمتر از 8 ساعت به درخواست شما پاسخ خواهیم داد.
* نتیجه بررسی از طریق ایمیل ارسال خواهد شد
شماره کارت : 6104337650971516 شماره حساب : 8228146163 شناسه شبا (انتقال پایا) : IR410120020000008228146163 بانک ملت به نام مهدی تاج دینی